00:00
04:04
There is currently no information available for this song.
(Ase Leumas, ma beat bwanji ase?)
Tolani Joker
Tolani Joker
Tolani Joker, Arasi tolani Joker
Inu tolani Joker
Isssh tolani Joker
Tolani Joker, Arasi tolani Joker
Tayibakasha
Tayibakasha
Tayibakasha
Eya tayibakasha
Eish tayibakasha
Tayibakasha
Tayibakasha
Iwe umatiii!
Ndangoponya pick two
Support, jump
Kuzaponya eight, reverse back
Eko ka flower, I want Nyashhh
Iwe tatola, knock, cards
Aliyense ali ndi Joker wake
Aliyense ali ndi Joker wake
Aliyense ali ndi Joker wake
Aliyense ali ndi Joker wake
(Iwe umatii!)
Ndangoponya pick two
Support, jump
Kuzaponya eight, reverse back
Iwe eko ka flower, I want Nyashhh
Iwe tatola, Knock, Cards
Yaa achina
Sopano?
Reverse, Jump, Knock
Bwino pali nthambo za shoko
Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko
Nda closer knock nkati
Tili bho utha Ku checker stat
Joker wanga sungamuone ali koyesa dress ya nkwati
Ndi woyaka koma alibe smoko
Shape ngati botolo la coco
Ndi ofewa anakulila ma stocko
Ndimamusoka ndekha wona nsoko
Ndi wa loyal Joker wangayi
Ndi wa local ngati Masayi
Ma guy amayesa kumutexta daily hie pansi pa hie
Iwe umatii!
Ndangoponya pick two
Support, jump
Kuzaponya eight, reverse back
Iwe eko ka flower, I want Nyashhh
Iwe tatola, knock, cards
Aliyense ali ndi Joker wake
Aliyense ali ndi Joker wake
Aliyense ali ndi Joker wake
Aliyense ali ndi Joker wake
Iwe umatii!
Ndangoponya pick two
Support, jump
Kuzaponya eight, reverse back
Iwe eko ka flower, I want Nyashhh
Iwe tatola, knock, cards
Sopano?
Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko
Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko
Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko